Pamene pali mwayi watsopano m’moyo, anthu amalota za “ine watsopano” ndikupanga zisankho.
Komabe, sikophweka kukhazikitsa zisankho ndi kumazichita.Awa ndi maupangiri ena pakupanga zisankho.
Mu mkanema Vesi ya Baibulo inayamba ndi Yakobo 1:25.
“Koma munthu amene amayang’anitsitsa lamulo langwiro limene limapereka ufulu, ndikupitiriza kulichita. . . . kuchita izo- Iye adzadalitsidwa mu zimene amachita.” Yakobo 1:25
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi