Nzeru yozindikira Mulungu amene
wabwera padziko lapansi m’thupi
ili m’Baibulo.
Chifukwa chake, kwa iwo amene
amafunsa kuti, “N’chifukwa chiyani
Atate Ahnsahnghong ali Mulungu,
Khristu amene anabwera kachiwiri?”
tiyenera kuwasonyeza chiphaso cha Mulungu, Baibulo.
Yesu anapereka moyo wosatha
kwa anthu amene amadya mkate
ndi kumwa vinyo pa Paskha.
Komabe, palibe amene anaisunga
kwa zaka pafupifupi 1,600 Pasika
itathetsedwa mu AD 325 pa
Msonkhano wa ku Nicaea.
Mu nthawi ya Mzimu Woyera,
Khristu Ahnsahnghong wapereka
moyo wosatha kudzera mu Paskha
wa Mpingo wa Mulungu.
Kotero, Iye ndi Mulungu amene
anameza imfa kwamuyaya ndi
vinyo wapamitsokwe.
“Musanthula m'malembo, popeza muyesa
kuti momwemo muli nao moyo wosatha;
ndipo akundichitira Ine umboni ndi iwo
omwewo; . . .”
Yohane 5:39
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi