Nthawi iliyonse tikayitanidwa ndi Mulungu, ngati titsatira mawu Ake pokhulupirira thandizo Lake, osati luso lathu, ndiye kuti Mulungu adzatipatsa mphamvu za Mzimu Woyera monga momwe Anaperekera kwa Mose ndi Gideoni.
Lero, Mpingo wa Mulungu umalalikira uthenga wabwino ndipo umafalikira padziko lonse lapansi chifukwa cha thandizo la Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi akumwamba.
Ndipo Yesu anadza nalankhula nao, nanena,
. . . mukani, phunzitsani anthu a mitundu yonse,
ndi kuwabatiza iwo m’dzina la Atate, ndi la Mwana,
ndi la Mzimu Woyera:
ndi kuwaphunzitsa, asunge zinthu zonse zimene
ndinakulamulani inu; ndipo onani, Ine ndili pamodzi ndi
inu masiku onse, kufikira chimaliziro cha nthawi ya pansi pano.
Mateyu 28: 18–20
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi