Khristu Ahnsahnghong-Yesu amene anabwera kachiwiri-watidziwitsa kuti Baibulo ndi buku limene limachitira umboni za Mulungu.
“. . . Atate wathu muli kumwamba . . “Mat 6:9
Yesu anatiphunzitsa zakupezeka kwa Mulungu Atate.
Mtumwi Paulo anatiphunzitsa za kupezeka kwa Mulungu Amayi.
“Koma Yerusalemu wa Kumwamba uli waufulu, ndiwo Amayi wathu.”Agal 4:26
Ngakhale kudzera mu mfundo ya chilengedwe, tikhoza kudziwa zakupezeka kwa Mulungu Amayi. Maluwa a fungo lokoma ndi mtundu wosangalatsa, mitengo yobiliwira yowongoka kulunjika kumwamba, mkango, mfumu ya m’khalango, Chiombankhanga, mbuye wa thambo, nsomba ya m’madera otentha, chitsanzo chosangalatsa cha m’nyanja, ndi mwana wokongola . . . Zonse zimapatsidwa moyo kudzera mwa amayi awo.
Ndiye, ndani amene amatipatsa moyo wauzimu?
Monga zamoyo zonse zimapatsidwa moyo kuchokera kwa amayi awo, moyo wauzimu umaperekedwa ndi Mulungu Amayi.
“Mzimu ndi mkwatibwi anena , ‘Idzani! Ndipo wakumva anene, Idzani! iye wakumva ludzu adze, iye wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi