Baibulo limachitira umboni
kuti anthu anachimwa kumwamba
ndipo anaponyedwa padziko
lapansi pano, ndiponso kuti Yesu
anabwera padziko lapansi kudzapereka
chikhululukiro cha machismo
kwa anthu kuti abwerere kumwamba.
Ichi ndi chifukwa chake
Yesu adadutsa m'mazunzo
ndi kufa pa mtanda.
Kulapa ndiko kubwerera kwa
Mulungu, ndipo kumatheka
mwa kusunga malamulo ndi
mapwando amene anakwaniritsidwa
kudzera mu nsembe ya Mulungu.
Yesu amene anabwera zaka
2,000 zapitazo, Yohane M’batizi,
ndi oyera mtima a Mpingo
woyambirira komanso Khristu
Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi
mu m’badwo wa Mzimu Woyera,
onse anatsindika kulapa.
Ndi chifukwa chakuti kulapa
ndi njira yokhayo
yobwerera kwa Mulungu.
Tikati kuti tilibe uchimo,
tidzinyenga tokha, ndipo
mwa ife mulibe choonadi.
Ngati tivomereza machimo athu,
ali wokhulupirika ndi wolungama
Iye, kuti atikhululukire machimo athu,
ndi kutisambitsa kutichotsera
chosalungama chilichonse.
Tikanena kuti sitidachimwe,
timuyesa Iye wonama, . . .
1 Yohane 1:8-10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi