Mulungu, Mlimi wauzimu, amafuna tirigu, osati namsongole kapena mankhusu.
Kuti anthu akhale tirigu amene Mulungu afuna ndi kulowa m’nkhokwe yakumwamba, tiyenera kukhala ndi chikhulupiriro chonse chochokera m’ntchito, osati kungolemekeza Mulungu ndi milomo yathu yokha.
Masiku ano, mpingo wonga tirigu umene umatsatira mawu a Mulungu ndi mpingo wa Mulungu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi