Yesu ananena kuti madzi a moyo
operekedwa pa Phwando la
Misasa ndi Mzimu Woyera wa
mvula yotsiriza. Mneneri
Zekariya, Ezekieli, ndi Mtumwi
Yohane anachitira umboni kuti
Mayi wa Kumwamba Yerusalemu,
amene amatchedwa Mpando
wachifumu wa Mulungu, ndiye
Gwero la madzi a moyo. Ndipo
iwo anachitira umboni kuti Iye
adzapereka moyo wosatha kwa
anthu mu nthawi ino ya Mzimu
Woyera.
Mpingo wa Mulungu
umakhulupirira mawu akuti, “Iye
amene adziwa Mulungu
adzalandira Mzimu Woyera wa
mvula yotsiriza.”
Akugwira ntchito ngati mlonda
kuti alengeze molondola kwa
anthu onse kuti ayenera kubwera
ndi kulandira chipulumutso
kuchokera kwa Khristu
Ahnsahnghong ndi Mulungu
Amayi, komanso kulandira
Mzimu Woyera wa mvula ya
masika pa Phwando la Misasa.
Koma chikondwerero cha Ayuda cha Misasa,
linayandikira…Koma tsiku lomaliza, lalikululo
la chikondwerero, Yesu anaimirira nafuula,
ndi kunena, Ngati pali munthu akumva ludzu,
adze kwa Ine, namwe. Iye wokhulupirira Ine,
monga chilembo chinati, Mitsinje ya madzi
amoyo idzayenda, kutuluka m'kati mwake.
Koma ichi anati za Mzimu, amene iwo
akukhulupirira Iye anati adzalandire
Yohane 7:2-39
Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena,
Idzani. Ndipo wakumva anene, Idzani.
Ndipo wakumva ludzu adze; iye wofuna,
atenge madzi a moyo kwaulere.
Chivumbulutso 22:17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi