Ngati thupi lathu litataya
madzi 1-2%, zingayambitse ludzu lalikulu.
Ngati thupi lathu litataya
12% ya madzi ake, limatha kufa.
Ichi ndi mthunzi wa
zomwe zili mu dziko lauzimu,
kusonyeza kuti madzi a moyo
ndi ofunikira pakutsitsimutsa miyoyo yathu.
Mzimu ndi Mkwatibwi
okha—Khristu Ahnsahnghong
ndi Mayi Akumwamba Yerusalemu
Watsopano—akhoza kupereka madz
i a moyo amene amatsitsimutsa anthu.
Ndiwo amene anatsanulira
Mzimu Woyera pa Pentekosite, monga
analoseredwa ndi mneneri Zekariya
ndi Ezekieli m’Chipangano Chakale
ndi mtumwi Yohane ndi
Paulo m’Chipangano Chatsopano.
Ndipo Mzimu ndi
mkwatibwi anena, Idzani.
Ndipo wakumva anene, Idzani.
Ndipo wakumva ludzu adze;
iye wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere.
Chivumbulutso 22:17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi