zaka zikwi ziwiri zapitazo, atumwi ndi oyera a Mpingo woyambirira anakhulupirira Yesu monga Mulungu chifukwa Iye anawalonjeza Ufumu wosatha wa Kumwamba kudzera mu Pangano Latsopano. Momwemonso, ziwalo za Mpingo wa Mulungu zimakhulupirira mwa Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Mulungu anagwira ntchito ndi mayina osiyana mu mibadwo yosiyana - monga Mulungu Atate Yehova, Mulungu Mwana Yesu, ndi Mulungu Mzimu Woyera Ahnsahnghong. Koma, Iwo ali amodzi ndi Mulungu yemweyo amene anapanga Pangano Latsopano, lomwe ndi chizindikiro cha Mulungu.
“Masiku akubwera,” akutero Yehova, “pamene ndidzachita pangano latsopano ndi Aisraelindiponso nyumba ya Yuda.” . . . “Ndidzayika lamulo langa mʼmitima mwawo ndi kulilemba mʼmaganizo mwawo. Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.” Yeremiya 31:31–33
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi