Pamene tidya thupi la Yesu’ ndi kumwa mwazi Wake kupyolera mu Paska, Yesu amakhala mwa ife, ndipo chotero, timatha kugawana chikondi Chake ndi aliyense amene takumana naye.
Lero, mamembala a Mpingo wa Mulungu alandira chikondi cha Paska wa pangano latsopano kuchokera kwa Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, ndipo akulalikira za chikondi cha Mulungu ku dziko lonse lapansi.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi