Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi nthawi zonse amatiphunzitsa kukondana wina ndi mnzake.
Kumbuyo kwa chiphunzitsochi, tingapeze mzimu wa Ubuntu umene ana a ku Africa ananena ndi liwu limodzi, “Ine ndiri chifukwa inu muli, ndipo ine ndiri chifukwa ife tiri.
Monga chonchi, mamembala a Mpingo wa Mulungu amalalikira uthenga wabwino wa ufumu, ndi chiyembekezo kuti anthu onse angathe kupita ku ufumu wa kumwamba pamodzi osati iwo okha.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi