Mulungu anamasula Mose ndi Aisrayeli ku Igupto ndi mphamvu ya Paska. Aisiraeli anali asanacite Pasika kwa zaka 38, koma anacita Pasika atangolowa m’dziko la Kanani. Kupyolera m’Paska wa pangano latsopano, Yesu mwiniyo anabwera napereka moyo wosatha kwa anthu. Kudzera m’zinthu zimenezi, titha kuona kuti Pasika ndi lamulo lofunika kwambiri limene anthu onse ayenera kuphunzira kwa makolo awo.
Lero, Khristu Ahnsahnghong anatiphunzitsanso Paska wa pangano latsopano, amene anali asanasungidwe kwa zaka 1,260, ndipo motsogozedwa ndi Mulungu Amayi, mamembala a Mpingo wa Mulungu padziko lonse lapansi akuisunga kukhala yopatulika. Izi zili choncho chifukwa dalitso lodabwitsa lakukhala ana a Mulungu lili pa Paska.
Ukakhala woyera ndi woongoka mtima, zoonadi adzakugalamukira tsopano, ndi kupindulitsa pokhala pako polungama. Ndipo chinkana chiyambi chako chinali chaching'ono, chitsiriziro chako chidzachuluka kwambiri.Pakuti ufunsire tsono mbadwo wapitawo, nusamalire zimene makolo ao adazisanthula.
Yobu 8:5-8
ophunzira anadza kwa Yesu, nati, Mufuna tikakonzere kuti Paska, kuti mukadye?... Yesu anatenga mkate… Tengani, idyani; ichi ndi thupi langa…. Mumwere ichi inu nonse pakuti ichi ndi mwazi wanga wa pangano wothiridwa chifukwa cha anthu ambiri ku kuchotsa machimo.
Mateyu 26:17-28
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi