Monga momwe Mfumu Yosiya ndi Mfumu Hezekiya anachotsa mafano onse ndi kutumikira Mulungu ndi mtima wonse ndi nzeru zawo zonse pamene anasunga Paska, leronso, titha kusunga lamulo loyamba lakuti, “Usakhale nayo milungu ina koma Ine,” pokhapo pa kusunga Paska wa Pangano Latsopano.
Ife, anthu, sitingapulumutsidwe kapena kudalitsidwa tikamatumikira milungu ina kusiya Mulungu. Ichi ndichifukwa chake Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi abwezeretsanso Paska wa Pangano Latsopano kudzera momwe tingatumikire Mulungu yekha, ndipo adatipempha kuti tizikondwerera.
Mchitireni Yehova Mulungu wanu Paska, monga mulembedwa m'buku ili la chipangano.
…Ndipo asanabadwe iye panalibe mfumu wolingana naye, imene inatembenukira kwa Yehova ndi mtima wake wonse, ndi moyo wake wonse, ndi mphamvu yake yonse,
2 Mafumu 23:21-25
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi