Tchimo la kudya zipatso za mtengo
wodziwitsa chabwino ndi choipa
unapatsiridwa anthu kuchokera
kwa Adamu ndi Heva m’munda wa Edeni.
Kuti anthu amasuke ku uchimo,
afunika choonadi cha mtengo
wa moyo umene umalola
amene amadya uwo
kukhala nawo moyo wosatha.
Ndi okhawo amene amazindikira nsembe
ndi chikondi cha Khristu Ahnsahnghong
ndi Amayi a Kumwamba, amene abweretsa
mtengo wa moyo, ndi kusunga choonadi
ichi ndi mtima wonse, akhoza
kumasulidwa ku uchimo wa imfa.
Tchimo la imfa, lomwe tinatengera
kwa Adamu, liyenera kuchotsedwa
kwa anthu amene akufuna
kupulumutsidwa ndi
kulowa mu ufumu wakumwamba.
Chotero, Khristu Ahnsahnghong anabwera
ku dziko lapansi kachiwiri nabweretsa Paska
wa pangano latsopano, choonadi cha mtengo
wa moyo, kukhululukira machimo aanthu onse
ndi kuwapatsa iwo cholowa cha ufumu wa kumwamba.
Ndipo ili ndi lonjezano
Iye anatilonjezera ife,
ndiwo moyo wosatha.
1 Yohane 2:25
Chifukwa chake Yesu anati kwa
iwo, Indetu, indetu, ndinena ndi inu,
Ngati simukudya thupi la Mwana wa
Munthu ndi kumwa mwazi wake,
mulibe moyo mwa inu nokha.
Iye wakudya thupi langa
ndi kumwa mwazi wanga
ali nao moyo wosatha; . . .
Yohane 6:53-54
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi