Mu munda wa Edeni, munali mtengo wa moyo, womwe unapereka moyo wosatha kwa iwo amene anadya zipatso zake. Koma chifukwa cha tchimo la Adamu ndi Heva, Mulungu anatseka njira ya ku mtengo wa moyo.
Popeza Mulungu yekha angatsegulenso njira ya ku mtengo wa moyo, zaka 2,000 zapitazo, Yesu anabwera kudzapatsa ochimwa moyo wosatha. Iye anabweretsa Paska wa pangano latsopano, amene tingadye ndi kumwa thupi ndi mwazi wa Yesu—zenizeni za mtengo wa moyo.
Komabe, mu AD 325, Paska inathetsedwa ndi Mfumu ya Roma Constantine. Kuti atsegulenso njira ya ku moyo wosatha, Mulungu anabwera padziko kachiwiri ali mu thupi. Iye ndi Khristu Ahnsahnghong.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi