Mulungu Elohim amene anadzitcha “Ife” analenga zakumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo masiku asanu ndi limodzi, anaimitsa kumanga kwa Nsanja ya Babele, ndipo anatumiza aneneri.
Mulungu Elohim, ndiko kuti, Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi, akhala akugwira ntchito yachiwombolo pamodzi kuyambira pa Chilengedwe, ndipo ngakhale m'badwo uno wa Mzimu Woyera, Iwo adakhazikitsa Mpingo wa Mulungu, adabwezeretsa choonadi, ndipo akupereka moyo wosatha kwa anthu kwaulere.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi