Mulungu anadalitsa tsiku la Sabata pa chiyambi ndipo
analipanga kukhala lopatulika, ndipo analiika kukhala
lachinayi la Malamulo Khumi m ‘nthawi ya Mose; tsiku
la Sabata ndilo lamulo la Mulungu limene tiyenera kusunga
kufikira chimaliziro cha nthawi ya pansi pano.
Yesu anatiphunzitsa kuti tiyenera kusunga tsiku la Sabata kukhala lopatulika mpaka mapeto a nthawi pa kunena kuti, “Pempherani kuti kuthawa kwanu kusadzachitike pa Sabata,” Choncho n ‘kulakwa kunena kuti palibe chifukwa chosungira tsiku la Sabata m’ nthawi ya Chipangano Chatsopano ndipo amasutsana ndi ziphunzitso za Yesu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi