Mamembala a Mpingo wa Mulungu Akuitanidwa ku Phwando la Ukwati wa Kumwamba
Zaka 2 sauzande zapitazo, Yesu anayerekezera chipulumutso chathu ndi kulowa mu ufumu wakumwamba ndi kuitanidwa ku phwando laukwati kuti kuchitire umboni za Amayi Akumwamba, amene adzaonekere ndi Mulungu Atate ndi kupereka madzi a moyo kwa anthu mu m'badwo wotsiriza wa Mzimu Woyera.
Pa kubwera koyamba kwa Yesu, nthawi inali isanafike kuti Mkwatibwi awonekere, kotero Mkwati,yekha ndi alendo anatchulidwa m’mafanizo a Yesu, koma Baibulo limalosela kuti Mkwatibwi, monga Mkazi wa Mwanawankhosa, amene ndi, Amayi Akumwamba, Yerusalemu Wakumwamba, adzaonekera m'masiku otsiriza.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi