Mulungu akulamula ana Ake kuti agawane fungo la Mulungu Mayi wina ndi mnzake. Mwana wobadwa kumene amada nkhaŵa akamalephera kumva mawu a mayi ake kapena kununkhiza fungo lawo. Momwemonso, miyoyo yathu singathe kupita ku ufumu wakumwamba ngati tisiya Mulungu Amayi.
“Fungo la mayi” limatanthauza mtima wokondana, woleza mtima, wosadzikuza, woganizira ena, wogwirizana, ndi wolemekeza abale ndi alongo ndi maganizo odzichepetsa.
Kupyolera mu Phwando la Misasa, ana anazindikira chikondi cha Amayi amene anazipereka nsembe kaamba ka chipulumutso cha anthu. Kwa iwo, Khristu Ahnsahnghong anachita chozizwitsa kuti miyoyo yambiri inabwerera ku Ziyoni.
Pakuti adakuitanani inu, abale, mukhale mfulu; chokhacho musachite nao ufulu wanu chothandizira thupi, komatu mwachikondi chitiranani ukapolo.
Agalatiya 5:13
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi