Mulungu walonjeza kuti adzatisakha kukhala mafumu mu ufumu wakumwamba. Kuti mtundu wa anthu uyende m’njira yoyenera monga mafumu mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, chimene chili chofunika ndicho chikhulupiriro kuchita mogwirizana ndi mawu Ake, osati m’lingaliro laumunthu koma la Mulungu.
Njira zonse zomwe zimawoneka zovuta, m’malingaliro aumunthu zinadzazidwadi ndi chikondi ndi madalitso tikamawona malingaliro a Mulungu. Choncho, mamembala a Mpingo wa Mulungu amayenda m’njira ya chikhulupiriro, n’kupanga mawu a m’Baibulo akuti, “Tsatirani kulikonse kumene Mulungu akutsogolera,” mfundo yawo yaikulu yotsogolera.
Pakuti maganizo anga sali maganizo anu, ngakhale
njira zanu sizili njira zanga, ati Yehova.Pakuti monga
kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, momwemo
njira zanga zili zazitali kupambana njira zanu,
ndi maganizo anga kupambana
maganizo anu.
Yesaya 55:8–9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi