Pa Phwando la Mkate Wopanda Chotupitsa, anthu onse ayenera kukumbukira chikondi cha Khristu pa nsembe ndi kuvutika pamtanda, kulapa machimo onse akale, ndi kupempha anthu kuti alape ndi choonadi cha chipulumutso chomwe Iye watipatsa.
Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, amene anabwera padziko lapansi mu thupi, anakhala moyo wa kulalikira, kuti, “Lapani, pakuti ufumu wakumwamba wayandikira.”
Mwa ichi, Iwo anasonyeza kuti moyo wodzipereka kulalikira ndi moyo wodalitsika umene umakwaniritsa kulapa kokongola.
Ndinena kwa inu, kotero kudzakhala chimwemwe Kumwamba chifukwa cha wochimwa mmodzi wotembenuka mtima, koposa anthu olungama makumi asanu ndi anai mphambu asanu ndi anai, amene alibe kusowa kutembenuka mtima. . . .
Chomwecho, ndinena kwa inu, kuti kumakhala chimwemwe pamaso pa angelo a Mulungu chifukwa cha munthu wochimwa mmodzi amene atembenuka mtima.
Luka 15:7–10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi