Kuti tidziwe ngati ntchito zathundi zolondola kapena zolakwika,tiyenera kubwera kwa Mulungu,amene ali kuunika koona.
Masiku ano, m’dziko lamdimakumene anthu sangathe kuzindikirachifuniro cha Mulungu,Khristu Ahnsahnghong ndiMulungu Amayi awunikirakuunika kwa chowonadicha moyo kudzera mu Sabata ndi Paska.
Mulungu anabwera ku dziko lapansingati kuunika, kugonjetsa mzimuwa dziko la mdima, kutiphunzitsaza zinthu zakumwamba, kubweretsachiyembekezo ku dziko lapansi,ndi kuwalitsa kuunika.Chimodzimodzi, ana aMulungu ayenera kuunikiransokuwala kwa Uthenga Wabwinokudziko lapansi kuti aliyense adziwe Mulungu.
[M]wa amene mulungu wa nthawi ino ya pansi pano anachititsa khungu maganizo ao a osakhulupirira, kuti chiwalitsiro cha Uthenga Wabwino wa ulemerero wa Khristu, amene ali chithunzithunzi cha Mulungu, chisawawalire. . . . Pakuti Mulungu amene anati, Kuunika kudzawala kutuluka mumdima, ndiye amene anawala m’mitima yathu kutipatsa chiwalitsiro cha chidziwitso cha ulemerero wa Mulungu pankhope pa Yesu Khristu. 2 Akorinto 4:4–6
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi