M'masiku a Sodomu ndi Gomora, akamwini a Loti anakumana ndi chionongeko chifukwa ankaona chenjezolo ngati nthabwala. Mneneri amene ananyalanyaza chenjezo la Mulungu anaphedwa momvetsa chisoni ndi mkango panjira. Mu nthawi ya Mose, oyamba kubadwa a m'banja lililonse la Ejipito amene sanasunge Paska anafa. Kudzera m'nkhani zakalezi, timaphunzira kumvetsera uthenga wochenjeza wa Mulungu m'badwo uno.
Khristu Ahnsahnghong anati, kusunga malamulo a Mulungu n'kukonda Mulungu. Anatiphunzitsanso kuti, monga mu nthawi ya Eksodo, pakusunga lamulo la Paska lokha tingalandire chizindikiro cha chipulumutso ku chionongeko ndi kukhala pansi pa chitetezo cha Mulungu pakati pa zionongeko zomaliza zonenenedweratu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi