Mfumu Solomo inanena kuti kuopa Mulungu ndi udindo wa anthu onse, ndipo Yesu ananena kuti lamulo lalikulu ndi kukonda Mulungu ndi mtima wathu wonse ndi nzeru zathu zonse.
Iye anakhazikitsa lamulo la pangano latsopano, ponena kuti chikondi ndicho kukwaniritsidwa kwa lamulo.
Mulungu anapachikidwa pamtanda chifukwa Amakonda kwambiri mtundu wa anthu.
Nyama zonse zimene zinaperekedwa nsembe malinga ndi lamulo la Chipangano Chakale zikuimira Mulungu, potsiriza umboni wa m’mene Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi athu a Kumwamba, amene anabwera mu m’badwo wa Mzimu Woyera, adzakhazikitsa pangano latsopano, kuphatikizapo tsiku la Sabata ndi Paska, kuti anthu apulumutsidwe.
Mau atha; zonse zamveka zatha;
opa Mulungu, musunge malamulo
ake; pakuti choyenera anthu
onse ndi ichi.
Mlaliki 12:13
Ananu, mverani akukubalani mwa
Ambuye, pakuti ichi nchabwino.
Lemekeza atate wako ndi amai
ako (ndilo lamulo loyamba
lokhala nalo lonjezano), kuti
kukhale bwino ndi iwe, ndi kuti
ukhale wa nthawi yaikulu padziko.
Aefeso 6:1–3
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi