Monga pali mabodza ambiri kutsanzira zopangidwa zapamwamba padziko lapansi, mipingo yabodza iliponso yochuluka. Kupeza mpingo woona kumene kuli chipulumutso, choyamba, dzina lake liyenera kukhala “Mpingo wa Mulungu,” chachiwiri, uyenera kukhazikitsidwa ndi Mulungu Mwini, ndipo chachitatu, uyenera kukhala ndi choonadi cha Baibulo.
Baibulo limasonyeza kuti mpingo woona umene unabwezeretsedwa ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amene ali Mzimu ndi Mkwatibwi, ndipo akusunga choonadi chonse kuphatikizapo tsiku la Sabata ndi Paska zimene Yesu anasunga, ndi Ziyoni, malo othawirako ndi chipulumutso chimene Mulungu wakonza.
Ndipo anadza ku Nazarete, kumene analeredwa; ndipo tsiku la Sabata analowa m’sunagoge, monga anazolowera, naimiriramo kuwerenga m’kalata. . . .
Luka 4:16
Paulo, woitanidwa akhale mtumwi wa Khristu Yesu mwa chifuniro cha Mulungu, ndi Sostene mbaleyo, kwa Mpingo wa Mulungu wakukhala mu Korinto, . . .
1 Akorinto 1:1–2
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi