Baibulo ndi aneneri anachitira umboni za chifukwa chimene Khristu adzabwere kachiwiri ndicho kudzawononga imfa, ndiko kuti, kupereka moyo wosatha kwa anthu, ndi kuwatengera ku ufumu wakumwamba.
Njira yokhayo kwa anthu, amene anachita tchimo loyenera imfa kumwamba, ndi kulandira moyo wosatha pakudya ndi kumwa thupi ndi mwazi wa Yesu kudzera mu Paska, monga momwe zinalili zaka 2,000 zapitazo.
Potengera ndi ulosi wa Yesaya kuti Mulungu yekha ndi amene angakonze phwando lomwe limameza imfa kwamuyaya, mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhulupirira Khristu Ahnsahnghong monga Mulungu ndipo amasunga Paska chifukwa Iye ndiye amene wawononga imfa kudzera mu Paska.
Iye wakudya thupi langa ndi
kumwa mwazi wanga ali nao
moyo wosatha; ndipo Ine
ndidzamuukitsa iye tsiku
lomaliza.
Yohane 6:54
Ndipo m'phiri limeneli Yehova wa
makamu adzakonzera anthu ake
onse phwando la zinthu zonona,
phwando la vinyo wa pamitsokwe
. . . Iye wameza imfa kunthawi
yonse; . . . Ndipo adzanena tsiku
limenelo, Taonani, uyu ndiye
Mulungu wathu; tamlindirira
Iye, adzatipulumutsa; . . .
Yesaya 25:6–9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi